Motivation and Inspiration Phyzix – Mwantinti

Phyzix – Mwantinti

Download Mwantinti Mp3 byย  Ft. Teddy Makadi & Pon G

A cool song performed by the Malawianย multi-award-winning & best-selling rapper, songwriter, performer & record producer โ€œ“, as this one is titled โ€œMwantintiโ€ featuring Teddy Makadi & Pon G. This song is sure to bless your heart and uplift your spirit.

Download Audio Mp3, Stream, Share, and be blessed

DOWNLOAD HERE

DOWNLOAD MORE PHYZIX SONGS HERE

You May Also Like: ๐Ÿ‘‡๐Ÿฝ

Lyrics: Mwantinti by

(INTRO: Phyzix, Teddy Makadi & Pon G)
Yeah
It’s Only Entertainment
Wole
Wala
Yeah/ Very Good Very Good

(VERSE 1: Phyzix & Teddy)
Kukukisa pang’ono ngati ka 2par/ unati ndisamasuke kwanu ndi koshupha/ ndikafika pa gate n’salize hooter/ ndizingolemba message mpanda uziwudumpha/ pena pake ndiwe ka mkazi kofuntha/ zomwe tikupangazi akwanu azandikuntha/ alibe nazo zoti ndine wotchuka/ zoti ndimaoneka pa TV pa luntha/

Ndi ka light skin girl ngati amarula
Body lining sanayuze ruler
Love language yake nnati dollar
Ine mayine koma sindilola
Let me take you to munalula
You rob my heart ndiwe Kawalala
Mmangofuna uzisangalala
Ma love obhebha ngati za mankhwala

(HOOK: Teddy Makadi & Pon G)
Mmh love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)

(VERSE 2: Phyzix & Teddy)
Zikukoma ngati nyama yakufupa/ battery la moyo wanga lafika pa full bar/ koma kwanu ati ndine kape ndine luga/ amandionera diso limodzi la Ruger/ I’m gonna represent you though I ain’t passed the bar/ baby girl I gotchu we gonna go far/ ngati Bluetooth devices tinalinka/ mami ndinu chida ndinu kilinka

Sumasunga tu ma secret mayine secret
Zimandiwaza zopita ku ma picnic
Tiye kunyanja ndikayiphula ticket
Na Iwe ndi ndi ndikumata Ti
Ati chikondi ndi mbo
Kondi ndi mbola
Kwa iyeyo bola ndimpatse zi dollar
Komabe ine love yako nde ndiyitola
Strictly lobola ndiyomwe uyiwona

(HOOK: Teddy Makadi & Pon G)
Mmh love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)

(VERSE 3: Phyzix)
Uzipola moto ukamandithoka/ uchepetse za mavuvu siwe motocar/ Zomwe ndimafuna utsanzike pochoka/ Nsanje zayamba kuchuluka mtima utchoka/ ndisaone kakape ka kukuthoka/ sindisekelera kakaka zopotoka/ ukafuna dollar trans ID kuti kha/ usamaope kupititsidwa ku chatinkha/ mkaziyu ndi wanga wa ine ndekha/ sitimaitana gulu potenga chindekha/ ndikati ndikugwa amandiwakha/ uyu nde ndimanyadila kuti ndinasankha/ Very Good

(BRIDGE: Pon G)
Ndikumva tseketseke ngati sugar (illovo)
Ngati kumaloto (Loto)
Hunnie!
You’re my Princess
Kukonda iwe sindipanga regret

(HOOK: Teddy Makadi & Pon G)
Mmh love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)

You May Also Like: ๐Ÿ‘‡๐Ÿฝ

1 COMMENT

Comment below with your feedback and thoughts on this post.